Skip to content
Malawian Sign Language Dictionary
Menu
Front page
Information
Foreword
Mawu otsogolera
Acknowledgements
Introduction
Mawu oyamba
Instructions for how to use the dictionary
References
Signs
Themes – Zotsogolerazi
Basic Conversation – Kulumikizana / Kuyankhulana
Family and people – Banja ndi Anthu
Emotions – Zomwe munthu akumva muntima zinthu zikamachitika
Time – Nthawi
Education – Maphunziro
Profession – Ntchito
Religion – Chipembedzo
Health – Zaumoyo
Colours – Makaka
Animals – Nyama
Sports – Masewero
Transport – Mayendedwe
Weather and Nature – Zanyengo ndi Zachilengedwe
Food and Drink – Zakudya ndi Zakumwa
Places – Malo
Other Everyday Signs – Zizindikiro zina
Alphabets – Alufabeti
Numbers – Manambala
Contact information
Menu
Sidebar
Signs
494
signs, displaying
217 - 228
:
217. Guard
-londera, -tchinjiriza, -teteza, -yang'anira, mlonda, odikira, olondera
218. nurse
namwino
219. tailoring
telala, -osoka zovala, -soka chinthu
220. carpenter, carpentry
Mpalamatabwa, konza zinthu za matabwa, kalipentala, Ukalipentala, ntchito yokonza ndi zinthu za matabwa
221. leader, lead
mtsogoleri, tsogolera
222. economic
zachuma
223. control
longosola
224. interview
-funsa mafunso ofufuza, -yesa mafunso
225. pray, religion, prayer
pemphera, chipembedzo, pemphero
226. God
Mulungu, Chauta
227. bless
dalitsa (kudalitsa)
228. bless
dalitsa (kudalitsa)
To top